1 Mafumu 21:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Choncho Ahabu analowa m’nyumba mwake ali wachisoni ndi wokhumudwa chifukwa cha mawu amene Naboti Myezereeli anamuuza, onena kuti: “Sindikupatsani cholowa cha makolo anga.” Ndiyeno anakagona pabedi lake n’kutembenukira kukhoma,+ ndipo sanadye chakudya. Salimo 2:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Tsopano inu mafumu, sonyezani kuzindikira,Lolani kuti maganizo anu akonzedwe, inu oweruza a dziko lapansi.+
4 Choncho Ahabu analowa m’nyumba mwake ali wachisoni ndi wokhumudwa chifukwa cha mawu amene Naboti Myezereeli anamuuza, onena kuti: “Sindikupatsani cholowa cha makolo anga.” Ndiyeno anakagona pabedi lake n’kutembenukira kukhoma,+ ndipo sanadye chakudya.
10 Tsopano inu mafumu, sonyezani kuzindikira,Lolani kuti maganizo anu akonzedwe, inu oweruza a dziko lapansi.+