Salimo 9:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+ Yesaya 26:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+
12 Pofunafuna okhetsa magazi,+ iye adzakumbukira ndithu anthu osautsidwa.+Sadzaiwala ndithu kulira kwawo.+
21 Pakuti taonani! Yehova akubwera kuchokera kumene amakhala kuti adzaimbe mlandu anthu okhala m’dzikoli.+ Magazi amene dzikoli linakhetsa lidzawaonetsa poyera,+ ndipo silidzabisanso anthu amene linapha.”+