Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 22:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Taona, udzabala mwana.+ Mwana ameneyo adzakhala munthu wabata, ndipo ndidzam’patsa mpumulo pakati pa adani ake onse omuzungulira.+ N’chifukwa chake dzina lake adzakhala Solomo,*+ ndipo m’masiku ake ndidzakhazikitsa mtendere+ ndi bata pa Isiraeli.

  • 1 Mbiri 28:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Ndipo pa ana anga onse (pakuti Yehova wandipatsa ana ambiri)+ anasankha mwana wanga Solomo+ kuti akhale pampando wachifumu+ wa ufumu wa Yehova, kuti alamulire Isiraeli.

  • Miyambo 21:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Palibe nzeru kapena kuzindikira kulikonse, kapena malangizo alionse otsutsana ndi Yehova.+

  • Danieli 2:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Iye amasintha nthawi ndi nyengo,+ amachotsa mafumu ndi kuika mafumu,+ amapereka nzeru kwa anthu anzeru ndiponso amachititsa kuti anthu ozindikira adziwe zinthu.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena