Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Miyambo 2:6
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 6 Pakuti Yehova amapereka nzeru.+ Kudziwa zinthu ndi kuzindikira kumatuluka m’kamwa mwake.+

  • Mlaliki 2:26
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 26 Munthu wabwino pamaso pa Mulungu,+ Mulunguyo amam’patsa nzeru, kudziwa zinthu, ndi kusangalala.+ Koma wochimwa amam’patsa ntchito yotuta ndi kusonkhanitsa zinthu kuti azipereke kwa munthu amene ali wabwino pamaso pa Mulungu woona.+ Zimenezinso n’zachabechabe ndipo kuli ngati kuthamangitsa mphepo.+

  • Aefeso 1:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 kuti Mulungu wa Ambuye wathu Yesu Khristu, Atate waulemerero, akupatseni mzimu wa nzeru+ ndi kuti mumvetse zimene Iye akuulula mogwirizana ndi kumudziwa molondola.+

  • Yakobo 1:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho ngati wina akusowa nzeru,+ azipempha kwa Mulungu,+ ndipo adzamupatsa,+ popeza iye amapereka mowolowa manja kwa onse ndiponso amapereka mosatonza.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena