1 Mafumu 15:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Pomalizira pake, Asa anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake.+ Ndiyeno Yehosafati+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake. 2 Mbiri 18:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ahabu mfumu ya Isiraeli anafunsa Yehosafati mfumu ya Yuda kuti: “Kodi upita nane ku Ramoti-giliyadi?”+ Yehosafati anamuyankha kuti: “Iwe ndi ine ndife amodzi. Anthu anga ndi anthu ako ndi amodzi, ndipo ali nawe limodzi pankhondoyi.”+
24 Pomalizira pake, Asa anagona ndi makolo ake+ ndipo anaikidwa m’manda pamodzi ndi makolo ake mu Mzinda wa Davide kholo lake.+ Ndiyeno Yehosafati+ mwana wake anayamba kulamulira m’malo mwake.
3 Ahabu mfumu ya Isiraeli anafunsa Yehosafati mfumu ya Yuda kuti: “Kodi upita nane ku Ramoti-giliyadi?”+ Yehosafati anamuyankha kuti: “Iwe ndi ine ndife amodzi. Anthu anga ndi anthu ako ndi amodzi, ndipo ali nawe limodzi pankhondoyi.”+