2 Mbiri 18:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Chotero mfumu ya Isiraeli inaitana nduna ya panyumba ya mfumu,+ n’kuiuza kuti: “Kaitane Mikaya mwana wa Imula, ndipo ubwere naye msangamsanga.”+
8 Chotero mfumu ya Isiraeli inaitana nduna ya panyumba ya mfumu,+ n’kuiuza kuti: “Kaitane Mikaya mwana wa Imula, ndipo ubwere naye msangamsanga.”+