1 Mafumu 22:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Chotero mfumu ya Isiraeli inaitana nduna ina ya panyumba ya mfumu,+ n’kuiuza kuti: “Kaitane Mikaya mwana wa Imula, ndipo ubwere naye msangamsanga.”+
9 Chotero mfumu ya Isiraeli inaitana nduna ina ya panyumba ya mfumu,+ n’kuiuza kuti: “Kaitane Mikaya mwana wa Imula, ndipo ubwere naye msangamsanga.”+