2 Mbiri 18:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mfumu ya Isiraeli itamva zimenezi inauza Yehosafati kuti: “Pajatu ndinakuuza kuti, ‘Adzalosera zoipa zokhudza ine, osati zabwino.’”+
17 Mfumu ya Isiraeli itamva zimenezi inauza Yehosafati kuti: “Pajatu ndinakuuza kuti, ‘Adzalosera zoipa zokhudza ine, osati zabwino.’”+