2 Mbiri 18:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pomalizira pake, mzimu+ wina unabwera kudzaima pamaso pa Yehova n’kunena kuti, ‘Ine ndikam’pusitsa.’ Ndipo Yehova anamufunsa kuti, ‘Ukam’pusitsa motani?’+
20 Pomalizira pake, mzimu+ wina unabwera kudzaima pamaso pa Yehova n’kunena kuti, ‘Ine ndikam’pusitsa.’ Ndipo Yehova anamufunsa kuti, ‘Ukam’pusitsa motani?’+