1 Mafumu 22:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pomalizira pake, mzimu wina+ unabwera kudzaima pamaso pa Yehova n’kunena kuti, ‘Ine ndikam’pusitsa.’ Ndipo Yehova anamufunsa kuti, ‘Ukam’pusitsa motani?’+
21 Pomalizira pake, mzimu wina+ unabwera kudzaima pamaso pa Yehova n’kunena kuti, ‘Ine ndikam’pusitsa.’ Ndipo Yehova anamufunsa kuti, ‘Ukam’pusitsa motani?’+