Numeri 16:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ngati anthuwa angafe mmene anthu onse amafera, ndipo ngati angalangidwe ndi chilango cha anthu,+ pamenepo, ndiye kuti sindinatumidwe ndi Yehova.+
29 Ngati anthuwa angafe mmene anthu onse amafera, ndipo ngati angalangidwe ndi chilango cha anthu,+ pamenepo, ndiye kuti sindinatumidwe ndi Yehova.+