2 Mbiri 18:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Akuluakulu oyang’anira asilikali okwera magaleta aja atangozindikira kuti si mfumu ya Isiraeli, nthawi yomweyo anasiya kumuthamangitsa ndipo anabwerera.+
32 Akuluakulu oyang’anira asilikali okwera magaleta aja atangozindikira kuti si mfumu ya Isiraeli, nthawi yomweyo anasiya kumuthamangitsa ndipo anabwerera.+