1 Mafumu 22:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Akuluakulu oyang’anira asilikali okwera magaleta aja atangozindikira kuti si mfumu ya Isiraeli, nthawi yomweyo anasiya kum’thamangitsa ndi kubwerera.+
33 Akuluakulu oyang’anira asilikali okwera magaleta aja atangozindikira kuti si mfumu ya Isiraeli, nthawi yomweyo anasiya kum’thamangitsa ndi kubwerera.+