Salimo 110:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+ Mateyu 25:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Adzaika nkhosa kudzanja lake lamanja,+ koma mbuzi adzaziika kumanzere kwake.+
110 Yehova wauza Ambuye wanga kuti:+“Khala kudzanja langa lamanja+Kufikira nditaika adani ako monga chopondapo mapazi ako.”+