2 Samueli 18:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Pamenepo Yowabu anati: “Ndisachedwe chonchi ndi iwe!” Atatero anatenga mikondo itatu m’manja mwake ndi kulasa+ nayo mtima wa Abisalomu ali ndi moyo+ pakati pa mtengo waukulu.
14 Pamenepo Yowabu anati: “Ndisachedwe chonchi ndi iwe!” Atatero anatenga mikondo itatu m’manja mwake ndi kulasa+ nayo mtima wa Abisalomu ali ndi moyo+ pakati pa mtengo waukulu.