1 Samueli 2:35 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 35 Pamenepo ndidzadziutsira wansembe wokhulupirika+ amene adzachita mogwirizana ndi zimene zili mumtima mwanga ndi zofuna zanga. Ndidzam’mangira nyumba* yokhalitsa, ndipo adzatumikira wodzozedwa wanga+ monga wansembe nthawi zonse. 1 Mbiri 6:53 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 53 Ahitubu anabereka Zadoki,+ ndipo Zadoki anabereka Ahimazi.+ 1 Mbiri 12:28 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 28 Panalinso Zadoki+ mnyamata wamphamvu ndi wolimba mtima ndi atsogoleri 22 a m’nyumba ya makolo ake. 1 Mbiri 16:39 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 39 Anasiyanso Zadoki+ wansembe ndi abale ake ansembe kuchihema cha Yehova chimene chinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni,+ 1 Mbiri 24:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Davide ndi Zadoki,+ yemwe anali wochokera mwa ana a Eleazara, ndiponso Ahimeleki,+ wochokera mwa ana a Itamara, anagawa ana a Aroniwo m’magulu a udindo pa utumiki wawo.+ Salimo 109:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Masiku a moyo wake akhale ochepa.+Udindo wake monga woyang’anira utengedwe ndi munthu wina.+
35 Pamenepo ndidzadziutsira wansembe wokhulupirika+ amene adzachita mogwirizana ndi zimene zili mumtima mwanga ndi zofuna zanga. Ndidzam’mangira nyumba* yokhalitsa, ndipo adzatumikira wodzozedwa wanga+ monga wansembe nthawi zonse.
28 Panalinso Zadoki+ mnyamata wamphamvu ndi wolimba mtima ndi atsogoleri 22 a m’nyumba ya makolo ake.
39 Anasiyanso Zadoki+ wansembe ndi abale ake ansembe kuchihema cha Yehova chimene chinali pamalo okwezeka a ku Gibeoni,+
3 Davide ndi Zadoki,+ yemwe anali wochokera mwa ana a Eleazara, ndiponso Ahimeleki,+ wochokera mwa ana a Itamara, anagawa ana a Aroniwo m’magulu a udindo pa utumiki wawo.+