-
1 Mafumu 2:38Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
38 Simeyi atamva zimenezi anauza mfumu kuti: “Mwanena bwino. Mmene mbuyanga mfumu mwanenera, ndi mmenenso mtumiki wanu achitire.” Ndipo Simeyi anakhala ku Yerusalemu masiku ambiri.
-