Miyambo 16:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kuchita zinthu zoipa kumanyansa mafumu,+ chifukwa mpando wachifumu umakhazikika ndi chilungamo.+ Mlaliki 8:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndikunena kuti: “Sunga lamulo la mfumu.+ Chita zimenezi polemekeza lumbiro la Mulungu.+