Miyambo 25:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Woipa akachotsedwa pamaso pa mfumu,+ mpando wake wachifumu udzakhazikitsidwa ndi chilungamo.+ Miyambo 29:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Mfumu ikamaweruza anthu onyozeka mwachilungamo,+ mpando wake wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.+ Chivumbulutso 19:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+
14 Mfumu ikamaweruza anthu onyozeka mwachilungamo,+ mpando wake wachifumu udzakhazikika mpaka kalekale.+
11 Ndipo nditayang’ana ndinaona kumwamba kutatseguka, kenako ndinaona hatchi yoyera.+ Wokwerapo wake dzina lake linali Wokhulupirika+ ndi Woona.+ Iyeyo anali kuweruza ndi kumenya nkhondo mwachilungamo.+