Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Genesis 43:30
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 30 Tsopano Yosefe anachokapo mofulumira chifukwa anagwidwa chifundo mumtima poona m’bale wakeyo.+ Anafunafuna malo oti akalirire, ndipo analowa m’chipinda chamkati n’kukagwetsa misozi.+

  • Oweruza 15:1
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Ndiyeno patapita nthawi, m’masiku okolola tirigu, Samisoni anapita kukaona mkazi wake uja, atatenga kamwana ka mbuzi.+ Pamenepo iye anati: “Ndilowa m’chipinda cha mkazi wanga.”+ Koma bambo a mkaziyo sanam’lole kuti alowe.

  • 2 Samueli 13:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Ndiyeno Aminoni anauza Tamara kuti: “Bweretsa chakudya chonditonthoza kuchipinda chogona kuti ndidye kuchokera m’manja mwako monga wodwala.” Pamenepo Tamara anatenga makeke amene anapangawo ndi kupita nawo kwa Aminoni m’bale wake m’chipinda chogona.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena