1 Mafumu 1:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti+ anadzikweza+ n’kumati: “Ineyo ndikhala mfumu yolamulira!”+ Kenako anapangitsa galeta* lake. Analinso ndi amuna okwera pamahatchi,* ndi amuna 50 amene ankathamanga patsogolo pake.+ 1 Mafumu 1:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Koma tsopano onani, Adoniya+ wakhala mfumu ndipo inu mbuyanga mfumu simukuzidziwa n’komwe zimenezi.+
5 Pa nthawi imeneyi Adoniya+ mwana wa Hagiti+ anadzikweza+ n’kumati: “Ineyo ndikhala mfumu yolamulira!”+ Kenako anapangitsa galeta* lake. Analinso ndi amuna okwera pamahatchi,* ndi amuna 50 amene ankathamanga patsogolo pake.+
18 Koma tsopano onani, Adoniya+ wakhala mfumu ndipo inu mbuyanga mfumu simukuzidziwa n’komwe zimenezi.+