Ekisodo 37:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Ndiyeno anapanga tebulo la mtengo wa mthethe,+ mikono iwiri m’litali, mkono umodzi m’lifupi ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.+ 2 Mbiri 4:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Solomo anapanga ziwiya zonse+ zimene zinali panyumba ya Mulungu woona, guwa lansembe lagolide,+ matebulo+ oikapo mkate wachionetsero,
10 Ndiyeno anapanga tebulo la mtengo wa mthethe,+ mikono iwiri m’litali, mkono umodzi m’lifupi ndi mkono umodzi ndi hafu msinkhu wake.+
19 Solomo anapanga ziwiya zonse+ zimene zinali panyumba ya Mulungu woona, guwa lansembe lagolide,+ matebulo+ oikapo mkate wachionetsero,