Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Ekisodo 25:37
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 37 Ndipo uchipangire nyale 7. Nyalezo ziziyatsidwa kuti ziziunikira patsogolo pake.+

  • Ekisodo 37:17
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 17 Kenako anapanga choikapo nyale+ chagolide woyenga bwino. Chimenechi chinali chosula. Choikapo nyalechi chinali ndi nthambi m’mbali mwake, ndiponso chinali ndi masamba ofunga duwa, mfundo ndi maluwa.+

  • Chivumbulutso 1:20
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 20 Koma za chinsinsi chopatulika cha nyenyezi 7,+ zimene waona m’dzanja langa lamanja, ndi za chinsinsi cha zoikapo nyale 7 zagolide,+ tanthauzo lake ndi ili: Nyenyezi 7, zikuimira angelo* a mipingo 7, ndipo zoikapo nyale 7, zikuimira mipingo 7.+

  • Chivumbulutso 2:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 “‘Choncho, kumbukira malo amene unali usanagwe, lapa+ ndi kuchita ntchito za poyamba. Ngati sutero, ndikubwera kwa iwe,+ ndipo ndidzachotsa choikapo nyale chako+ pamalo ake ngati sulapa.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena