Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Mbiri 29:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Kenako Davide anatamanda+ Yehova pamaso pa mpingo wonse,+ kuti: “Mudalitsike+ inu Yehova Mulungu wa Isiraeli+ atate wathu, kuyambira kalekale mpaka kalekale.

  • 2 Mbiri 6:4
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 4 Mfumuyo inapitiriza kuti: “Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ amene analankhula ndi pakamwa pake kwa Davide bambo anga,+ ndipo ndi manja ake wakwaniritsa+ zimene ananena, kuti,

  • Nehemiya 9:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Choncho Yesuwa, Kadimiyeli, Bani, Hasabineya, Serebiya, Hodiya, Sebaniya ndi Petahiya, omwe anali Alevi, anati: “Dzukani, tamandani+ Yehova Mulungu wanu kuyambira kalekale mpaka kalekale.*+ Inu Mulungu wathu, anthuwa atamande dzina lanu laulemerero,+ lokwezeka kuposa dalitso ndi chitamando chilichonse.

  • Salimo 41:13
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 13 Adalitsike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+

      Kuyambira kalekale mpaka kalekale.+

      Ame! Ame!*+

  • Luka 1:68
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 68 “Atamandike Yehova Mulungu wa Isiraeli,+ chifukwa wacheukira anthu ake+ ndi kuwapatsa chipulumutso.+

  • Chivumbulutso 4:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 “Ndinu woyenera, inu Yehova* Mulungu wathu wamphamvu,+ kulandira ulemerero+ ndi ulemu,+ chifukwa munalenga zinthu zonse,+ ndipo mwa kufuna kwanu,+ zinakhalapo ndipo zinalengedwa.”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena