2 Mbiri 6:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 “Anthu anu Aisiraeli akagonja kwa mdani wawo+ chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno akabwerera+ kwa inu n’kutamanda dzina lanu+ ndi kupemphera+ ndiponso kupempha kuti muwachitire chifundo pamaso panu m’nyumba ino,+
24 “Anthu anu Aisiraeli akagonja kwa mdani wawo+ chifukwa choti anali kukuchimwirani,+ ndiyeno akabwerera+ kwa inu n’kutamanda dzina lanu+ ndi kupemphera+ ndiponso kupempha kuti muwachitire chifundo pamaso panu m’nyumba ino,+