Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Yobu 7:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Choncho, ine sinditseka pakamwa panga.

      Ndilankhula chifukwa cha kuvutika mumtima,+

      Ndilankhula za nkhawa zanga, chifukwa moyo wanga ukupweteka.

  • Salimo 73:21
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 21 Pakuti mtima unandipweteka+

      Ndipo ndinamva ululu mu impso zanga.+

  • Miyambo 14:10
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 10 Mtima umadziwa kuwawa kwa moyo wa munthu,+ ndipo mlendo sangalowerere pamene mtimawo ukusangalala.

  • Aroma 7:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Munthu wovutika ine! Ndani adzandipulumutse ku thupi limene likufa imfa imeneyi?+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena