Aroma 6:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Pakuti tikudziwa kuti umunthu wathu wakale unapachikidwa pamodzi ndi iye pamtengo,+ kuti thupi lathu lauchimo likhale ngati lakufa,+ kuti tisapitirize kukhala akapolo a uchimo.+ Aroma 8:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Koma ngati Khristu ali wogwirizana ndi inu,+ ngakhale kuti thupi ndi lakufa chifukwa cha uchimo, mzimu ndiwo moyo+ chifukwa cha chilungamo.
6 Pakuti tikudziwa kuti umunthu wathu wakale unapachikidwa pamodzi ndi iye pamtengo,+ kuti thupi lathu lauchimo likhale ngati lakufa,+ kuti tisapitirize kukhala akapolo a uchimo.+
10 Koma ngati Khristu ali wogwirizana ndi inu,+ ngakhale kuti thupi ndi lakufa chifukwa cha uchimo, mzimu ndiwo moyo+ chifukwa cha chilungamo.