Ekisodo 20:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musaope, chifukwa Mulungu woona wabwera+ kuti akuyeseni, ndi kuti mupitirizebe kumuopa kuti musachimwe.”+ Deuteronomo 6:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Muyenera kuphunzira zimenezi kuti muziopa+ Yehova Mulungu wanu, n’cholinga choti masiku onse a moyo wanu muzisunga mfundo zake ndi malamulo ake amene ndikukuuzani, inuyo, ana anu ndi zidzukulu zanu,+ ndiponso kuti masiku anu atalike.+ Miyambo 8:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+
20 Pamenepo Mose anauza anthuwo kuti: “Musaope, chifukwa Mulungu woona wabwera+ kuti akuyeseni, ndi kuti mupitirizebe kumuopa kuti musachimwe.”+
2 Muyenera kuphunzira zimenezi kuti muziopa+ Yehova Mulungu wanu, n’cholinga choti masiku onse a moyo wanu muzisunga mfundo zake ndi malamulo ake amene ndikukuuzani, inuyo, ana anu ndi zidzukulu zanu,+ ndiponso kuti masiku anu atalike.+
13 Kuopa Yehova kumatanthauza kudana ndi zoipa.+ Ndimadana ndi kudzikweza, kunyada,+ njira yoipa ndiponso pakamwa ponena zopotoka.+