Ekisodo 19:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+ Deuteronomo 9:26 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+ Deuteronomo 32:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Pamene Wam’mwambamwamba anapereka cholowa kwa mitundu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,+Anaika malire a anthu+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+
5 Tsopano ngati mudzalabadiradi+ mawu anga ndi kusunga pangano langa,+ pamenepo mudzakhaladi chuma changa chapadera pakati pa anthu ena onse,+ chifukwa dziko lonse lapansi ndi langa.+
26 Pamenepo ndinayamba kupembedzera+ Yehova ndi kunena kuti, ‘Yehova Ambuye Wamkulu Koposa, musawononge anthu anu, amene ndiwo chuma chanu chapadera,+ anthu amene munawawombola ndi mphamvu yanu, amene munawatulutsa mu Iguputo+ ndi dzanja lamphamvu.+
8 Pamene Wam’mwambamwamba anapereka cholowa kwa mitundu,+Pamene analekanitsa ana a Adamu,+Anaika malire a anthu+Poganizira chiwerengero cha ana a Isiraeli.+