1 Mafumu 4:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Iye ankalamulira chilichonse kumbali yakuno ya Mtsinje,+ kuchokera ku Tifisa mpaka ku Gaza.+ Ankalamulira mafumu onse a mbali yakuno ya Mtsinje,+ ndipo m’zigawo zake zonse munali mtendere.+ 2 Mbiri 14:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Kenako anamanga mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri m’dziko la Yuda,+ chifukwa m’dzikolo munalibe chosokoneza chilichonse, komanso palibe anachita naye nkhondo pa zaka zimenezi, chifukwa Yehova anam’patsa mpumulo.+ Aheberi 4:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Ife amene tasonyeza chikhulupiriro tikulowadi mu mpumulowo. Ponena za mpumulo umenewu iye anati: “Choncho ndinalumbira+ mu mkwiyo wanga kuti, ‘Sadzalowa+ mu mpumulo wanga,’”+ ngakhale kuti ntchito zake zinali zitatha+ kuyambira pamene dziko linakhazikitsidwa.*+
24 Iye ankalamulira chilichonse kumbali yakuno ya Mtsinje,+ kuchokera ku Tifisa mpaka ku Gaza.+ Ankalamulira mafumu onse a mbali yakuno ya Mtsinje,+ ndipo m’zigawo zake zonse munali mtendere.+
6 Kenako anamanga mizinda yokhala ndi mipanda yolimba kwambiri m’dziko la Yuda,+ chifukwa m’dzikolo munalibe chosokoneza chilichonse, komanso palibe anachita naye nkhondo pa zaka zimenezi, chifukwa Yehova anam’patsa mpumulo.+
3 Ife amene tasonyeza chikhulupiriro tikulowadi mu mpumulowo. Ponena za mpumulo umenewu iye anati: “Choncho ndinalumbira+ mu mkwiyo wanga kuti, ‘Sadzalowa+ mu mpumulo wanga,’”+ ngakhale kuti ntchito zake zinali zitatha+ kuyambira pamene dziko linakhazikitsidwa.*+