Salimo 86:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+ Salimo 119:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Ndithandizeni kuti mtima wanga uziganizira zikumbutso zanu,+Osati kupeza phindu.*+ 2 Atesalonika 3:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Ambuye apitirize kutsogolera mitima yanu kuti muzikonda+ Mulungu ndi kuti muzipirira+ chifukwa cha Khristu.
11 Inu Yehova, ndilangizeni za njira yanu.+Ndidzayenda m’choonadi chanu.+Ndipatseni mtima wosagawanika kuti ndiope dzina lanu.+
5 Ambuye apitirize kutsogolera mitima yanu kuti muzikonda+ Mulungu ndi kuti muzipirira+ chifukwa cha Khristu.