2 Mbiri 8:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Kumapeto kwa zaka 20+ zimene Solomo anamanga nyumba ya Yehova+ ndi nyumba yake,+ Mlaliki 2:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndinachita zinthu zikuluzikulu.+ Ndinadzimangira nyumba zambirimbiri.+ Ndinalima minda ya mpesa yambirimbiri.+
4 Ndinachita zinthu zikuluzikulu.+ Ndinadzimangira nyumba zambirimbiri.+ Ndinalima minda ya mpesa yambirimbiri.+