2 Mbiri 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anapereka nsembe yopsereza+ kwa Yehova paguwa lansembe+ la Yehova limene iye anamanga patsogolo pa khonde.+
12 Panali pa nthawi imeneyi pamene Solomo anapereka nsembe yopsereza+ kwa Yehova paguwa lansembe+ la Yehova limene iye anamanga patsogolo pa khonde.+