1 Mafumu 6:38 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 38 Ndipo m’chaka cha 11, m’mwezi wa Buli,* womwe ndi mwezi wa 8, anamaliza+ kumanga zinthu zonse panyumbayo motsatira mapulani ake onse.+ Motero, Solomo anatha zaka 7 akumanga nyumbayo. 2 Mbiri 8:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Choncho ntchito yonse ya Solomo, kuyambira pa tsiku limene anayala+ maziko a nyumba ya Yehova kufikira pamene inatha,+ inayenda bwino. Motero nyumba ya Yehova inatha kumangidwa.+
38 Ndipo m’chaka cha 11, m’mwezi wa Buli,* womwe ndi mwezi wa 8, anamaliza+ kumanga zinthu zonse panyumbayo motsatira mapulani ake onse.+ Motero, Solomo anatha zaka 7 akumanga nyumbayo.
16 Choncho ntchito yonse ya Solomo, kuyambira pa tsiku limene anayala+ maziko a nyumba ya Yehova kufikira pamene inatha,+ inayenda bwino. Motero nyumba ya Yehova inatha kumangidwa.+