Genesis 28:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Kenako, malowo anawatcha Beteli.+ Koma dzina lakale la mzindawo linali Luzi.+ Yoswa 16:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Malire a gawo+ la ana a Yosefe+ anayambira kumtsinje wa Yorodano+ kufupi ndi Yeriko kukafika kumadzi a Yeriko chakum’mawa, mpaka kuchipululu chochokera ku Yeriko kukafika kudera lamapiri la Beteli.+ 1 Samueli 7:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Chaka ndi chaka Samueli anali kuzungulira m’madera a Beteli,+ Giligala+ ndi Mizipa,+ ndipo anali kuweruza+ Isiraeli m’malo onsewa. 1 Mafumu 12:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Ndiyeno chifaniziro cha ng’ombe chimodzi anakachiika ku Beteli,+ china anakachiika ku Dani.+
16 Malire a gawo+ la ana a Yosefe+ anayambira kumtsinje wa Yorodano+ kufupi ndi Yeriko kukafika kumadzi a Yeriko chakum’mawa, mpaka kuchipululu chochokera ku Yeriko kukafika kudera lamapiri la Beteli.+
16 Chaka ndi chaka Samueli anali kuzungulira m’madera a Beteli,+ Giligala+ ndi Mizipa,+ ndipo anali kuweruza+ Isiraeli m’malo onsewa.