Ekisodo 20:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+ Oweruza 6:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Komanso ndinakuuzani kuti: “Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Musaope milungu ya Aamori+ amene mukukhala m’dziko lawo.”+ Koma inu simunamvere mawu anga.’”+
4 “Usadzipangire fano kapena chifaniziro cha chinthu chilichonse chakumwamba, kapena chapadziko lapansi, kapenanso cham’madzi a padziko lapansi.*+
10 Komanso ndinakuuzani kuti: “Ine ndine Yehova Mulungu wanu.+ Musaope milungu ya Aamori+ amene mukukhala m’dziko lawo.”+ Koma inu simunamvere mawu anga.’”+