Deuteronomo 11:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Chotero muzisunga mosamala malangizo onse ndi zigamulo zonse+ zimene ndikuika pamaso panu lero.+