Yesaya 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Tsopano ubetcherane+ ndi mbuye wanga mfumu ya Asuri,+ ndipo ine ndikupatsa mahatchi 2,000 kuti ndione ngati iweyo ungathe kupeza okwerapo.+
8 Tsopano ubetcherane+ ndi mbuye wanga mfumu ya Asuri,+ ndipo ine ndikupatsa mahatchi 2,000 kuti ndione ngati iweyo ungathe kupeza okwerapo.+