Yesaya 36:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Ndiye ubetcherane ndi mbuye wanga, mfumu ya Asuri+ ndipo ine ndikupatsa mahatchi 2,000 kuti tione ngati iweyo ungathe kupeza okwerapo. Yesaya Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 36:8 Yesaya 1, ptsa. 386-387
8 Ndiye ubetcherane ndi mbuye wanga, mfumu ya Asuri+ ndipo ine ndikupatsa mahatchi 2,000 kuti tione ngati iweyo ungathe kupeza okwerapo.