Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Deuteronomo 28:53
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 53 Pamenepo udzadya chipatso cha mimba yako, mnofu wa ana ako aamuna ndi ana ako aakazi,+ amene Yehova Mulungu wako wakupatsa, chifukwa cha zovuta ndi nsautso zimene adani ako adzakupanikiza nazo.

  • 2 Mafumu 6:25
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 25 Patapita nthawi, mu Samariya+ munagwa njala yaikulu. Asiriyawo anapitirizabe kuzungulira mzindawo mpaka mtengo wogulira mutu wa bulu+ unafika pa ndalama 80 zasiliva, ndipo zitosi za nkhunda+ zodzaza manja awiri* mtengo wake unafika pa ndalama zisanu zasiliva.

  • Ezekieli 4:15
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 15 Choncho iye anandiuza kuti: “Chabwino, ndikupatsa ndowe za ng’ombe m’malo mwa tudzi touma ta anthu kuti uphikirepo chakudya chako.”

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena