2 Mbiri 32:11 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 11 Hezekiyatu+ akungokunyengererani+ kuti mufe ndi njala ndi ludzu pokuuzani kuti: “Yehova Mulungu wathu atipulumutsa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+ Yesaya 36:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Koma Rabisake anayankha kuti: “Kodi mbuye wanga wandituma kuti ndidzanene mawuwa kwa mbuye wanu yekha ndi kwa inuyo? Kodi sananditumenso kwa amuna amene akhala pamakomawo, kuti adye chimbudzi chawo ndi kumwa mkodzo wawo limodzi nanu?”+
11 Hezekiyatu+ akungokunyengererani+ kuti mufe ndi njala ndi ludzu pokuuzani kuti: “Yehova Mulungu wathu atipulumutsa m’manja mwa mfumu ya Asuri.”+
12 Koma Rabisake anayankha kuti: “Kodi mbuye wanga wandituma kuti ndidzanene mawuwa kwa mbuye wanu yekha ndi kwa inuyo? Kodi sananditumenso kwa amuna amene akhala pamakomawo, kuti adye chimbudzi chawo ndi kumwa mkodzo wawo limodzi nanu?”+