2 Mafumu 18:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma Rabisake anawayankha kuti: “Kodi mbuye wanga wandituma kuti ndidzanene mawuwa kwa mbuye wanu yekha ndi kwa inuyo? Kodi sananditumenso kwa amuna amene akhala pamakomawo, kuti adye chimbudzi chawo+ ndi kumwa mkodzo wawo limodzi nanu?”+
27 Koma Rabisake anawayankha kuti: “Kodi mbuye wanga wandituma kuti ndidzanene mawuwa kwa mbuye wanu yekha ndi kwa inuyo? Kodi sananditumenso kwa amuna amene akhala pamakomawo, kuti adye chimbudzi chawo+ ndi kumwa mkodzo wawo limodzi nanu?”+