1 Mafumu 8:29 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 29 Maso anu akhale akuyang’ana+ nyumba ino usiku ndi usana. Akhale akuyang’ana malo amene munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala kumeneko,’+ kuti mumvere pemphero limene mtumiki wanu akupemphera atayang’ana kumalo ano.+ Salimo 31:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Tcherani khutu lanu kwa ine.+Ndilanditseni mofulumira.+Mukhale thanthwe lolimba kwa ine,+Mukhale nyumba ya mpanda wolimba kuti mundipulumutse.+ Salimo 65:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Inu Wakumva pemphero, anthu a mitundu yonse adzabwera kwa inu.+
29 Maso anu akhale akuyang’ana+ nyumba ino usiku ndi usana. Akhale akuyang’ana malo amene munanena kuti, ‘Dzina langa lidzakhala kumeneko,’+ kuti mumvere pemphero limene mtumiki wanu akupemphera atayang’ana kumalo ano.+
2 Tcherani khutu lanu kwa ine.+Ndilanditseni mofulumira.+Mukhale thanthwe lolimba kwa ine,+Mukhale nyumba ya mpanda wolimba kuti mundipulumutse.+