2 Samueli 22:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Mulungu wanga ndiye thanthwe langa.+ Ine ndidzathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga+ ya chipulumutso ndi malo anga okwezeka achitetezo.+Iye ndi malo anga othawirako,+ Mpulumutsi wanga.+ Mumandipulumutsa ku chiwawa.+ Salimo 18:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Yehova ndiye thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso Wopereka chipulumutso kwa ine.+Mulungu wanga ndiye thanthwe langa. Ine ndidzathawira kwa iye.+Iye ndiye chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso ndiponso ndiye malo anga okwezeka achitetezo.+ Salimo 94:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Koma Yehova adzakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndipo Mulungu wanga adzakhala thanthwe langa lothawirako.+
3 Mulungu wanga ndiye thanthwe langa.+ Ine ndidzathawira kwa iye,Iye ndi chishango changa,+ nyanga* yanga+ ya chipulumutso ndi malo anga okwezeka achitetezo.+Iye ndi malo anga othawirako,+ Mpulumutsi wanga.+ Mumandipulumutsa ku chiwawa.+
2 Yehova ndiye thanthwe langa, malo anga achitetezo ndiponso Wopereka chipulumutso kwa ine.+Mulungu wanga ndiye thanthwe langa. Ine ndidzathawira kwa iye.+Iye ndiye chishango changa, nyanga* yanga ya chipulumutso ndiponso ndiye malo anga okwezeka achitetezo.+
22 Koma Yehova adzakhala malo anga okwezeka ndiponso achitetezo,+Ndipo Mulungu wanga adzakhala thanthwe langa lothawirako.+