Deuteronomo 28:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Udzadalitsika pa zochita zako zonse.+ Salimo 121:8 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 8 Yehova adzakuteteza pa zochita zako zonse,+Kuyambira tsopano mpaka kalekale.+ Miyambo 5:21 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 21 Pakuti njira za munthu zili pamaso pa Yehova,+ ndipo iye amaonetsetsa njira zake zonse.+