Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 1 Samueli 25:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Nthawi yomweyo, Abigayeli+ anafulumira kutenga mitanda 200 ya mkate, mitsuko iwiri ikuluikulu ya vinyo,+ anapha nkhosa zisanu,+ anatenganso miyezo ya seya* isanu ya tirigu wokazinga,+ mphesa zouma zoumba pamodzi 100+ ndi nkhuyu zouma zoumba pamodzi 200+ ndi kuzikweza pa abulu.

  • 1 Samueli 30:12
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 12 Anamupatsanso chidutswa cha nkhuyu zouma zoumba pamodzi ndi zidutswa ziwiri za mphesa zouma zoumba pamodzi.+ Iye anadya ndipo anapezanso mphamvu,+ chifukwa sanadye mkate kapena kumwa madzi kwa masiku atatu, usana ndi usiku.

  • 1 Mbiri 12:40
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 40 Ndiponso anthu onse apafupi ndi kumeneko, mpaka kumadera a Isakara,+ Zebuloni,+ ndi Nafitali,+ anali kubweretsa chakudya pa abulu,+ ngamila, nyulu* ndi ng’ombe. Anabweretsa zakudya zophikidwa ndi ufa.+ Anabweretsanso nkhuyu zouma zoumba pamodzi,+ mphesa zouma zoumba pamodzi,+ vinyo,+ mafuta,+ ng’ombe,+ ndi nkhosa.+ Anabweretsa zimenezi zambirimbiri, popeza mu Isiraeli munali chisangalalo+ chachikulu.

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena