Yesaya 39:4 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 4 Ndiyeno Yesaya anafunsa kuti: “Aona chiyani m’nyumba mwanu?”+ Hezekiya anayankha kuti: “Aona chilichonse chimene chili m’nyumba mwanga. Palibe chimene sindinawaonetse pa chuma changa.”
4 Ndiyeno Yesaya anafunsa kuti: “Aona chiyani m’nyumba mwanu?”+ Hezekiya anayankha kuti: “Aona chilichonse chimene chili m’nyumba mwanga. Palibe chimene sindinawaonetse pa chuma changa.”