2 Mafumu 20:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Ndiyeno Yesaya anafunsa kuti: “Aona chiyani m’nyumba mwanu?” Hezekiya anayankha kuti: “Aona chilichonse chimene chili m’nyumba mwanga. Palibe chimene sindinawaonetse pa chuma changa.”+
15 Ndiyeno Yesaya anafunsa kuti: “Aona chiyani m’nyumba mwanu?” Hezekiya anayankha kuti: “Aona chilichonse chimene chili m’nyumba mwanga. Palibe chimene sindinawaonetse pa chuma changa.”+