1 Mbiri 3:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Yotamu anabereka Ahazi,+ Ahazi anabereka Hezekiya,+ Hezekiya anabereka Manase,+ 2 Mbiri 33:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Manase+ anali ndi zaka 12 pamene anayamba kulamulira, ndipo analamulira zaka 55 ku Yerusalemu.+ Mlaliki 10:16 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 16 Dziko iwe, kodi zidzakuthera bwanji ngati mfumu yako ili kamnyamata,+ ndipo akalonga ako amangokhalira kudya ngakhale m’mawa? Mateyu 1:10 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 10 Hezekiya anabereka Manase.+Manase+ anabereka Amoni.+Amoni+ anabereka Yosiya.
16 Dziko iwe, kodi zidzakuthera bwanji ngati mfumu yako ili kamnyamata,+ ndipo akalonga ako amangokhalira kudya ngakhale m’mawa?