Yoswa 24:24 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 24 Ndiyeno anthuwo anamuyankha Yoswa kuti: “Tizitumikira Yehova Mulungu wathu ndi kumvera mawu ake!”+ 2 Mbiri 34:32 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 32 Kuwonjezera apo, mfumuyo inachititsa onse amene anali ku Yerusalemu ndi ku Benjamini kuti avomereze panganolo. Anthu okhala ku Yerusalemuwo anachita mogwirizana ndi pangano la Mulungu, Mulungu wa makolo awo.+ Yeremiya 4:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+
24 Ndiyeno anthuwo anamuyankha Yoswa kuti: “Tizitumikira Yehova Mulungu wathu ndi kumvera mawu ake!”+
32 Kuwonjezera apo, mfumuyo inachititsa onse amene anali ku Yerusalemu ndi ku Benjamini kuti avomereze panganolo. Anthu okhala ku Yerusalemuwo anachita mogwirizana ndi pangano la Mulungu, Mulungu wa makolo awo.+
2 Ndipo ngati udzalumbira+ kuti, ‘Pali Yehova Mulungu wamoyo, Mulungu wachoonadi+ ndi chilungamo,’+ pamenepo mitundu ya anthu idzapeza madalitso* kudzera mwa iye ndipo idzadzitama m’dzina lake.”+